Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zoonatu mwazi wanu wa miyoyo yanu ndidzafuna; pa dzanja la zinyama zonse ndidzaufuna: ndi pa dzanja la munthu, pa dzanja la mbale wace wa munthu ndidzaufuna moyo wa munthu.

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:5 nkhani