Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Mulungu, Ici ndici cizindikiro ca pangano limene ndipangana ndi Ine ndi inu, ndi zamoyo zonse ziti pamodzi ndi inu, ku mibadwo mibadwo;

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:12 nkhani