Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 9:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakhazikitsa pangano langa pamodzi ndi inu; zamoyo zonse sizidzamarizidwanso konse ndi madzi a cigumula; ndipo sikudzakhalanso konse cigumula cakuononga dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 9

Onani Genesis 9:11 nkhani