Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za mbalame monga mwa mitundu yao, ndi zinyama monga mwa mitundu yao, ndi zokwawa zonse za dziko lapansi monga mwa mitundu yao, ziwiri ziwiri monga mwa mitundu yao, zidzadza kwa iwe kuti zikhale ndi moyo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 6

Onani Genesis 6:20 nkhani