Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 47:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nthawi inayandikira kuti Israyeli adzafa, ndipo anaitana Yosefe mwana wace wamwamuna, nati kwa iye, Ngati ndapeza ufulu pamaso pako, ikatu dzanja lako pansi pa ncafu yanga, nundicitire ine zabwino ndi zoona: usandiikatu ine m'Aigupto;

Werengani mutu wathunthu Genesis 47

Onani Genesis 47:29 nkhani