Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 45:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamfotokozera iye kuti, Yosefe akali ndi moyo, ndipo alamulira m'dziko lonse la Aigupto, Pamenepo mtima wace unakomoka, pakuti sanawakhulupirira iwo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 45

Onani Genesis 45:26 nkhani