Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 44:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yosefe anauza tsanyumba wace kuti, Dzaza matumba a anthuwo ndi cakudya, monga angathe kunyamula, ndi kuika ndalama za yense kukamwa kwa thumba lace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 44

Onani Genesis 44:1 nkhani