Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 43:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anati, Munthuyo anafunsitsa za ife, ndi za abale athu, kuti, Atate wanu alipo? Kodi muli ndi mphwanu? ndipo tinamfotokozera iye monga mwa mau amenewo: ngati tinadziwa kuti iye adzati, Idzani naye mphwanu?

Werengani mutu wathunthu Genesis 43

Onani Genesis 43:7 nkhani