Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 43:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mawagawira mitanda ya patsogolo pace; koma mtanda wa Benjamini maposa mitanda ya onsewo kasanu. Ndipo anamwa, nasekera pamodzi ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Genesis 43

Onani Genesis 43:34 nkhani