Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 42:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo atate wao anati kwa iwo, Munandilanda ine ana; Yosefe palibe, Simeoni palibe, ndipo mudzacotsa Benjamini: zonse zimene zandigwera.

Werengani mutu wathunthu Genesis 42

Onani Genesis 42:36 nkhani