Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 42:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthuyo mwini dziko anati kwa ife, Momwemu ndidzadziwa kuti muli anthu oona; siyani mmodzi wa abale anu pamodzi ndi ine, tengani tirigu wa njala ya kwanu, mukani;

Werengani mutu wathunthu Genesis 42

Onani Genesis 42:33 nkhani