Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Ine ndine Farao, ndipo popanda iwe palibe munthu ali yense adzatukula dzanja lace kapena mwendo wace m'dziko lonse la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:44 nkhani