Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Farao ndipo anati kwa Yosefe, Ine ndalota loto, koma palibe wondimasulira; ndipo ndamva alikunena za iwe kuti, ukamva loto udziwa kumasulira.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:15 nkhani