Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 41:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Farao anatumiza nakaitana Yosefe; ndipo anamturutsa iye msanga m'dzenjemo: ndipo iye anameta, napindula malaya ace, nalowa kwa Farao.

Werengani mutu wathunthu Genesis 41

Onani Genesis 41:14 nkhani