Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 40:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

akali masiku atatu Farao adzatukula mutu wako, nadzabwezera iwe nchito yako; ndipo udzapereka cikho ca Farao m'dzanja lace, monga kale lomwe m'mene unali wopereka cikho cace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 40

Onani Genesis 40:13 nkhani