Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwamunayo anadziwa mkazi wace Hava: ndipo anatenga pakati, nabala Kaini, ndipo anati, Ndalandira munthu kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Genesis 4

Onani Genesis 4:1 nkhani