Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 39:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anaitana amuna a m'nyumba yace, nanena ndi iwo kuti, Taonani, walowetsa kwa ife Mhebri kuti atiseke ife, analowa kwa ine kugona ndi ine, ndipo ndinapfuula ndi mau akuru:

Werengani mutu wathunthu Genesis 39

Onani Genesis 39:14 nkhani