Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 37:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abale ace ndipo anati kwa iye, Kodi udzakhala mfumu yathu ndithu? kapena udzatilamulira ife ndithu kodi? ndipo anamuda Iye koposa cifukwa ca maloto ace ndi mau ace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 37

Onani Genesis 37:8 nkhani