Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 35:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yakobo anati kwa a banja lace, ndi kwa onse amene anali ndi iye, Cotsani milungu yacilendo iri mwa inu, mudziyeretse, ndi kupindula zobvala zanu:

Werengani mutu wathunthu Genesis 35

Onani Genesis 35:2 nkhani