Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 35:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anati kwa Yakobo, Nyamuka nukwere kunka ku Beteli nukhale kumeneko: numange kumeneko guwa la nsembe la Mulungu amene anaonekera kwa iwe pamene unathawa ku nkhope ya Esau mbale wako.

Werengani mutu wathunthu Genesis 35

Onani Genesis 35:1 nkhani