Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati kwa Rakele, Kodi mpacabe kuti iwe wacotsa mwamuna wanga? Kodi ufuna kucotsanso mankhwala a mwana wanga? Rakele ndipo anati, Cifukwa cace iye adaagona nawe usiku uno cifukwa ca mankhwala a mwana wako.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:15 nkhani