Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 30:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rubeni ananka masiku akudula tirigu, napeza zipatso za mankhwala a cikondi m'thengo, nazitengera kwa amace Leva, Ndipo Rakele anati kwa Leya, Undipatseko mankhwala a mwana wako.

Werengani mutu wathunthu Genesis 30

Onani Genesis 30:14 nkhani