Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 28:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yakobo ndipo anauka m'mamawa, natenga mwala umene anaika pansi pa mutu wace, nauimiritsa, nathira mafuta pamtu pace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 28

Onani Genesis 28:18 nkhani