Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 27:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali atakalamba Isake, ndi maso ace anali a khungu losaona nalo, anamuitana Esau mwana wace wamwamuna wamkuru, nati kwa iye, Mwana wanga; ndipo anati kwa iye, Ndine pano.

Werengani mutu wathunthu Genesis 27

Onani Genesis 27:1 nkhani