Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 25:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakula anyamatawo; ndipo Esau anali munthu wakudziwa zakusaka nyama, munthu wa m'thengo; ndipo Yakobo anali munthu wofatsa, wakukhala m'mahema.

Werengani mutu wathunthu Genesis 25

Onani Genesis 25:27 nkhani