Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 25:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pambuyo pace ndipo anabadwa mphwace ndipo dzanja lace linagwira citende ca Esau, ndi dzina lace linachedwa Yakobo: ndipo Isake anali wa zaka makumi asanu ndi limodzi pamene mkazi wace anabala iwo.

Werengani mutu wathunthu Genesis 25

Onani Genesis 25:26 nkhani