Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 23:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munda wa Efroni umene unali m'Makipela, umene unali patsogolo pa Mamre, munda ndi phanga liri momwemo, ndi mitengo yonse inali m'mundamo, yokhala m'malire monse mozungulira momwemo,

Werengani mutu wathunthu Genesis 23

Onani Genesis 23:17 nkhani