Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 23:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anamvera Effoni, ndipo Abrahamu anamuyesera Efroni ndalama zimene ananena alinkumva ana a Heti, masekele a siliva mazana anai, ndalama zomwezo agulana nazo malonda.

Werengani mutu wathunthu Genesis 23

Onani Genesis 23:16 nkhani