Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 22:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Isake ananena ndi Abrahamu atate wace, nati, Atate wanga; ndipo iye anati, Ndine pano, mwana wanga. Ndipo anati, Taonani moto ndi nkhuni; koma mwana wa nkhosa wa nsembe yopsereza ali kuti?

Werengani mutu wathunthu Genesis 22

Onani Genesis 22:7 nkhani