Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Tengatu mwana wako, wamwamuna wayekhayo, Isake, amene ukondana naye, numuke ku dziko la Moriya; numpereke iye kumeneko nsembe yopsereza pa limodzi la mapiri lomwe ndidzakuuza iwe.

Werengani mutu wathunthu Genesis 22

Onani Genesis 22:2 nkhani