Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu anatukula maso ace nayang'ana taonani, pambuyo pace nkhosa yamphongo yogwiridwa ndi nyanga zace m'ciyangoyangomo; ndipo ananka Abrahamu nakatenga nkhosa yamphongoyo, naipereka nsembe yopsereza m'malo mwa mwana wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 22

Onani Genesis 22:13 nkhani