Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 21:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abrahamu ananka mtengo wabwemba pa Beereseba, naitanira pamenepo dzina la Yehova, Mulungu wa nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 21

Onani Genesis 21:33 nkhani