Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anamtsegula m'maso mwace, ndipo anaona citsime ca madzi; namuka nadzaza mcenje ndi madzi, nampatsa mnyamata kuti amwe.

Werengani mutu wathunthu Genesis 21

Onani Genesis 21:19 nkhani