Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 21:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu anamva mau a mnyamatayo, ndi mthenga wa Mulungu anamuitana Hagara, ndi mau odzera kumwamba, nati kwa iye, Watani Hagara? usaope; cifukwa Mulungu anamva mau a mnyamata kumene ali.

Werengani mutu wathunthu Genesis 21

Onani Genesis 21:17 nkhani