Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati, Taonanitu, ambuye anga, tembenukanitu, kulowa m'nyumba mwa kapolo wanu, mugone usiku wonse, mutsuke mapazi anu, ndipo mudzalawira m'mawa kunka ulendo wanu. Ndipo anati, lai; koma tigone m'khwalalamu usiku wonse.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:2 nkhani