Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 19:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka Loti nanena nao akamwini ace amene anakwata ana ace akazi, nati, Taukani, turukani m'malo muno; popeza Yehova adzaononga mudziwu; koma akamwini ace anamyesa wongoseka.

Werengani mutu wathunthu Genesis 19

Onani Genesis 19:14 nkhani