Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pangano langa ndidzalimbikitsa ndi Isake, amene Sara adzakubalira iwe nthawi yomwe yino caka camawa.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:21 nkhani