Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi anai kudza zisanu ndi zinai, Yehova anamuonekera Abramu nati kwa iye, Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse; yenda iwe pamaso panga, nukhale wangwiro.

Werengani mutu wathunthu Genesis 17

Onani Genesis 17:1 nkhani