Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sarai anati kwa Abramu, Kusauka kwanga kukhale pa iwe: ndakupatsa iwe mdzakazi wanga pamtima pako; ndipo pakuona kuti anatenga pakati anandipeputsa ine m'maso mwace: Yehova aweruze pakati pa iwe ndi ine.

Werengani mutu wathunthu Genesis 16

Onani Genesis 16:5 nkhani