Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 16:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sarai mkazi wace wa Abramu anatenga Hagara mdzakazi wace wa ku Aigupto, Abramu atakhala m'dziko la Kanani zaka khumi, nampereka iye kwa Abramu mwamuna wace, kuti akhale mkazi wace.

Werengani mutu wathunthu Genesis 16

Onani Genesis 16:3 nkhani