Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 15:18-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Tsiku lomwelo Yehova anapangana cipangano ndi Abramu, nati, Ndidzapatsa mbeu zako dziko ili, kuyambira pa nyanja ya Aigupto kufikira pa nyanja yaikuru, nyanja ya Firate:

19. Akeni ndi Akenizi, Akadimoni, ndi Ahiti, ndi Aperezi, ndi Arefai, ndi Aamori, ndi Akanani, ndi Agirigasi, ndi Ajebusi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 15