Pamene anamva Abramu kuti mphwace anagwidwa, anaturuka natsogolera anyamata ace opangika, obadwa kunyumba kwace, mazana atatu kudza khumi ndi asanu ndi atatu, nawalondola kutikira ku Dani.