Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 11:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abramu ndi Nahori, anadzitengera okha akazi; dzina lace la mkazi wa Abramu ndilo Sarai; ndi dzina lace la mkazi wa Nahori ndilo Milika, mwana wace wa Harana, atate wace wa Milika, ndi atate wace wa Yisika.

Werengani mutu wathunthu Genesis 11

Onani Genesis 11:29 nkhani