Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Mulungu, Taonani, ndakupatsani inu therere lonse lakubala mbeu liri pa dziko lapansi, ndi mitengo yonse m'mene muli cipatso ca mtengo wakubala mbeu; cidzakhala cakudya ca inu:

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:29 nkhani