Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu ndipo anadalitsa iwo, ndipo adati kwa iwo, Mubalane, mucuruke, mudzaze dziko lapansi, muligonjetse: mulamulire pa nsomba za m'nyanja, ndi pa mbalame za m'mlengalenga, ndi pa zamoyo zonse zakukwawa pa dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:28 nkhani