Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:17-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Mulungu ndipo adaika zimenezo m'thambo la kumwamba, kuti ziunikire pa dziko lapansi,

18. nizilamulire usana ndi usiku, nizilekanitse kuyera ndi mdima: ndipo anaona Mulungu kuti kunali kwabino.

19. Ndipo panali madzulo ndipo panali m'mawa, tsiku lacinai.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1