Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati Mulungu, Madzi abale zocuruka zamoyo zoyendayenda, ndi mbalame ziuluke pamwamba pa dziko lapansi ndi pamlengalenga.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:20 nkhani