Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Genesis 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko lapansi linamera maudzu, therere lobala mbeu monga mwa mtundu wace, ndi mtengo wakubala zipatso, momwemo muli mbeu yace, monga mwa mtundu wace; ndipo anaona Mulungu kuti kunali kwabwino.

Werengani mutu wathunthu Genesis 1

Onani Genesis 1:12 nkhani