Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 8:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Inenso ndidzacita mwaukali; diso langa silidzalekerera, osawacitira cifundo Ine; ndipo cinkana apfuula m'makutu mwanga ndi mau akulu, koma sindidzawamvera ine.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 8

Onani Ezekieli 8:18 nkhani