Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezekieli 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo akupulumuka anu adzandikumbukila Ine kwa amitundu kumene anatengedwa ndende, kuti ndasweka ndi mtima wao wacigololo wolekana ndi Ine, ndi maso ao acigololo akutsata mafano ao; ndipo iwo adzakhala onyansa pamaso pao pa iwo eni, cifukwa ca zoipa anazicita m'zonyansa zao zonse.

Werengani mutu wathunthu Ezekieli 6

Onani Ezekieli 6:9 nkhani